Yowinila by Needn Ame Lyrics
Hook [Wishes Flexy]
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)
Verse [Wishes Flexy]
Ine ndimayaka bho
Ngati sitichila osandimenyala call
Ine siwa kwanu siwa kwanu siya cup
Mabodza ako unatingela kwanu siya cap
Usiye cap!!
Ulendo waku bawa subwera ndi receipt
Nyimbo yako mphwanga simabwera ndi repeat
Nkazi wako satha kumva kuti azipita
Azinzake ayamba kundifilaso kwambiri
Mesa ine ndine trapadi
Ndiye ndima player ngati lampard
Nyimbo zili pa sell ngati wankati
Akakhala special nde ndimwamadi
Hook [Wishes Flexy]
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)
Verse [Needn Ame]
When I need a new destiny I'm ending up on my level
That's a big time gangster with pollar water in his vessel
Who tried to detoxify but that had to get old
That had to get old what's better than a slim toast
What's better than a slim toast in this cold world
Break a bottle to the waste like my own belt
Few down for dead soliders run it run it
I need a little twitch in my mind where's my rabbit rabbit
Let the river run no baptism yeah
I'm sticking to my guns no sarcasm ey
Every portal I pop has to rain on me
Let me repuzzle if there's a massage in the bottle then it was meant for me
Hook [Wishes Flexy]
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)
Verse [Wishes Flexy]
Ine ndimayaka bho
Ngati sitichila osandimenyala call
Ine siwa kwanu siwa kwanu siya cup
Mabodza ako unatingela kwanu siya cap
Usiye cap!!
Ulendo waku bawa subwera ndi receipt
Nyimbo yako mphwanga simabwera ndi repeat
Nkazi wako satha kumva kuti azipita
Azinzake ayamba kundifilaso kwambiri
Mesa ine ndine trapadi
Ndiye ndima player ngati lampard
Nyimbo zili pa sell ngati wankati
Akakhala special nde ndimwamadi
Hook [Wishes Flexy]
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)
Verse [Needn Ame]
When I need a new destiny I'm ending up on my level
That's a big time gangster with pollar water in his vessel
Who tried to detoxify but that had to get old
That had to get old what's better than a slim toast
What's better than a slim toast in this cold world
Break a bottle to the waste like my own belt
Few down for dead soliders run it run it
I need a little twitch in my mind where's my rabbit rabbit
Let the river run no baptism yeah
I'm sticking to my guns no sarcasm ey
Every portal I pop has to rain on me
Let me repuzzle if there's a massage in the bottle then it was meant for me
Hook [Wishes Flexy]
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)
MAKWACHA EH AMANDISATA
ULENDO WAKUMOWA INEYO SINDIZATSALA
KOMA NDIKU DINTILA ( EH)
PALIBESO KU TSINILA (EH)
IYI MFANA NDIYOWINILA (EH)
ONA MENE NDIKUTHIMILA (EH)
USAMACHITE KUSILILA (EH)