Anakonza by Mastol Lyrics
*Pre-hook*
Kuwala kwako ngakhale dzuwa limayimika manja//
N'naponda potani kuti iweyo ukhale wanga//
Analenga nyenyezi ndi dzuwa,ndi amene analenga iwe//
Ndifunitsitsa tikathere pa guwa,mtima wanga watenga ndiwe//
*Verse 1*
Mtima wanga unasweka zinatsala ndi zidutswa//
Nde nkhani za chikondi ndimazileka zizidutsa//
Sindinkafuna olo kumva n'nasanduka gonthi//
Mu mtima munadzadza ndi milandu ngati khothi//
Ena ankaunena mtima wanga ati ndiwo-//
Vuta kuwukonda mwina umafila aunt Tiwo//
Anzanga mmawashisha akafusa ngati ndiwo//
Anapangitsa kuti ine ndizikhalabe single//
Ntakumana ndiwe dziko linayamba kuzuna//
Anthu anadziwa mtumwi wapeza ka tsuna//
Thupi losala-LA ngati sadwala Malungo//
She a Catholic,mfana wa Aroma moti nnafera fungo//
Ndapezadi sindingachite makaniso//
Mtimau mwatengadi sindingasinthe maganizo//
Ndaona kuwala kwako nde ndavomereza sure//
Olenga iwe analengaso nyenyezi ndi dzuwa//

*HOOK*
Na iwe Anakonza
(Na iwe anakonza)
Sanalakwitse anakonza
(Na iwe Anakonza)
Na iwe Anakonza
(Na iwe anakonza)
Sanalakwitse anakonza
(Na iwe Anakonza)
*Verse 2*
Anakonza inuyo mami eeh ndi kadaulo//
Ntchito anayigwira palibe dandaulo//
Monga Khristu akondera church mmau a Paulo//
Nane nzakukonda choncho kukusiya ndi malaulo//
Ndi kokongoletsa nde chikondi ndikatapila//
Musandivuwule mtima mwake ndikakamila//
Structure ya fine ngati clay soil//
Kubhebha sikuchepa olo asinthe hairstyle//
Mmmh Beiby nzakutengera ku nkopola//
Kukusintha dzina udzakhala mayi Topola//
Tiye kwanu konko tikalipire ya Lobola//
Kutsimikiza kuti palibe ozandisomphola//
Ndili nawe plan ma//
Ndikaona maso ake othwanima//
(maso akewo)
Tsemwe ndikudziwa kuti yemwe//
Analenga nyenyezi analenga ndiwe wemwe//

*Bridge*
Ine ndakonda iwe wekha//
Kukusiya ndi Zosatheka//
I swear there is nobody better//
Yahweh Anakonza iwe//

Na iwe Anakonza Beiby