Song Page - Lyrify.me

Lyrify.me

Galimoto by Lawi Lyrics

Genre: pop | Year: 2020

[Chorus]
Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto)

[Verse 1]
Ndimayenda wapasi ine eh-eh
Minga zimandibaya ine eh-eh
Anthu akandiona ine eh-eh
Amayamba kuseka ine eh-eh

[Refrain]
Kodi dona yambwana iyo (Siyo)
Kubayika ndi minga iyo (Siyo)
Ngati makobidi kulibe kwawoko (Siyo)
Ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh

[Chorus]
Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto)
Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala)
Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto)
[Verse 2]
Poti bambo ndinu namalamba mimbayi ndi umboni
M'mudzima nkhani akamakamba siyose ili miseche
Muli ndi galimoto mumakwera mukafuna
Nane ndi galimoto ndingathetse zolankhula

[Refrain]
Kodi dona yambwana iyo (Siyo)
Kubayika ndi minga iyo (Siyo)
Ngati makobidi kulibe kwawoko (Siyo)
Ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh

[Bridge]
Sho sho, pee-pee
Fumbi kuti lakata
Sho sho, ka-kata boom, kata-kata bumba
Vrrm, vrrm, pha
Vrrm, vrrm-vrrm, pha

[Refrain]
Kodi dona yambwana iyo (Siyo)
Kubayika ndi minga iyo (Siyo)
Ngati makobidi kulibe kwawoko (Siyo)
Ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh

[Chorus]
(Sho sho, pee-pee, sho)