Song Page - Lyrify.me

Lyrify.me

Chifundo Nane by Lawi Lyrics

Genre: pop | Year: 2021

[Intro]
Ayy
Chifundo nane
Chifundo nane
Oh, Chifundo nane
Chifundo nane
Chifundo nane
Chifundo nane
Mtima wanga don't you worry
Everything is gonna be alright

[Chorus]
Ambuye ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Mtima wanga sudera nkhawa
Chifukwa ali ndi chifundo nanee
Ine mtima wanga sudera nkhawa (Oh no)
Chifukwa ali ndi chifundo nane
[Verse 1]
Machimo anga ndi ambirimbiri osawerengeka ndipo
Mutazindikira zamumtima mwanga mukhoza kumandisala
Mutha kufuna kundimangilira ndikundiponya mu m'ndende
Ndizokoma kundiweruza, nzovuta kundimvetsetsa
Ndiye amene anandipanga amandidziwa
Zinsinsi zangazi pamaso pake ndizosabisika
Koma ngakhale ndimachimwa iye andikondabe
Amatsegura manja ake ndi kundikumbatira

[Chorus]
Oh, ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nanе
Mtima wanga sudera nkhawa
Chifukwa ali ndi chifundo nanee
Ine mtima wanga sudera nkhawa (Oh no)
Chifukwa ali ndi chifundo nanе (Oh, yeah)

[Verse 2]
Ayi-yayi-yayi
Ayi, ndachoka kutali, moyo wanga ndi umboni
Wandimenyera nkhondo, ndangokhala chete
Pomwe adani anga andikumbira mitsinje
Wandimangira mlatho, ndayenda powuma
Wandifewetsera zolimba zanga
[Chorus]
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ali ndi chifundo nane
Ine mtima wanga (Sudera nkhawa chifukwa ali ndi chifundo nane)
Ine mtima wanga (Sudera nkhawa
Chifukwa ali ndi chifundo nane)