Mamuna Amene Ndili by Kelvin Sings (MW) Lyrics
[Verse 1]
Unandipeza ndili lova, ndilibe kalikonse
Matumba mwanga mobowoka, nyumba yopanda khonde
Ndekuti dzuwa likawomba, katukuma kumaonda
Iweyo utandiwona, simvetsa chomwe unakonda
Utabwera unadilimbikitsa nati ndisabwelere m'mbuyo
Chomwe chinali chako naneso ndichanga kuti ndisamasowe tulo
[Pre-Chorus]
You must be insane to something
How could you give it all in thats nothing in return now, yah
[Chorus]
Ndikusowa chonena ine (Malangizo ako)
Andifikitsa pena ine (Poti ndine wako)
Bwera umunyadile mamuna amene ndili kamba ka iwe
Bwera umunyadile mamuna amene ndili kamba ka iweyo
[Verse 2]
For I was able enough, yeah
I had room for you my love
Ndizizwa ndichisankho chako (Chokhala nane 'khale mnyumba mwanga mpando munalibemo)
Pomwe sizinkandiyendela (Yendela)
Unagwada ndikupemphera (Pemphera)
Pamene mwayi unatetela, unandiwuza ndimukumbuke Namalenga
Ndikamabwera kuwulenje m'malo mwa nyama ndi denje
Kumandilandilabe ndi chimwemwe, ine pakamwa kakasi
You know pena nkati ndidye flas
Most of my days I minded the weather
But I believe God gave you to me to help me keep it together
[Pre-Chorus]
You must be insane to something
How could you give it all in thats nothing in return, now, yah

(Sinditha kumvetsetsa)
(Nkhawa zonse unathetsa)

(sim'mamvetsa mammie, kumvetsa mommie)

(Sindikanakwanitsa ndekha, ndeka)

([?])
[Outro]
Ndikusowa chonena ine
Malangizo ako, andifikitsa pena ine
Poti ndine wako

Eh, yeah