Song Page - Lyrify.me

Lyrify.me

Kuyambila Lero by Kelvin Sings (MW) Lyrics

Genre: pop | Year: 2021

[Verse 1]
Ndinafatsa kulingalira ine, baby
Nkhawa inandigwira ine, ine, ah
Mandalitso onsewa dziwa amasawutsa mtima wanga
Komwe kuli kokuya sikomwe ndinaponya mbedza yanga

[Pre-Chorus]
Koma ndazindikira kuti kunja konseku palibe angandikonde ngati iwe
Kundimvetsa ngati iwe
Nkona ndidza kwa iwe

[Chorus]
Chikondichi ndi chako, chako, chako
Mtimawu ndi wako, wako, wako
Udziwe kuyambila lero, yeah
Udziwe kuyambila lero, yeah
Zonsezi ndi zako, zako, zako
Mtimawu ndi wako, wako, wako
Ukamagona usiku wa lero, yeah
Udziwe kuyambila lero
[Verse 2]
Eko mtima wanga utenge
Palibe wina angawusamale bwino
Chauta nkhawa zathu ansenze
Palibe wina angazichengete bwino
Nde kuli konse tikafika (Kafika)
Nyengo zathu zizasintha (Zasintha)
Koma ndiyambe nkupepesa
(Pepa darly ndinaswa mtima wako)

[Pre-Chorus]
Koma ndazindikira kuti kunja konseku palibe angandikonde ngati iwe
Kundimvetsa ngati iwe
Nkona ndidza kwa iwe

[Chorus]
Chikondichi ndi chako, chako, chako
Mtimawu ndi wako, wako, wako
Udziwe kuyambila lero, yeah
Udziwe kuyambila lero, yeah
Zonsezi ndi zako, zako, zako
Mtimawu ndi wako, wako, wako
Ukamagona usiku wa lero, yeah
Udziwe kuyambila lero

[Bridge]
Chikondichi ndi chako, baby iwe
Mtimawu ndi wako
Kuyambila lero
Kuyambila lero
Udziwe kuyambila lero
[Chorus]
Chikondichi ndi chako, chako, chako
Mtimawu ndi wako, wako, wako
Udziwe kuyambila lero, yeah
Udziwe kuyambila lero, yeah
Zonsezi ndi zako, zako, zako
Mtimawu ndi wako, wako, wako
Ukamagona usiku wa lero, yeah
Udziwe kuyambila lero