Song Page - Lyrify.me

Lyrify.me

Mantha by Kelvin Sings Lyrics

Genre: rb | Year: 2018

VERSE 1
I made a choice
To sing for you
Nnapanga chisankho
Choyombila inu baba

Had an identity crisis
Was a little indecisive
Dziko lapansi linditaye
Kenako mundiwankhe
Zofuna zanga mundipase
Kenako ndikuthaweni

Ndinkati zizakhala chonchi
Mpaka liti abale
Chondiopsya ndichimodzi
Mulungu atati andiiwale

So I had to change my ways
Cause I got numbered days
Ndinatenga baibulo
Nawelenga ndipo salimo lidati
Chorus

Ndingayende muchigwa cha nthuzi waimfa sindiopa
(Waimfa sindiopa)
Wankati ali mwaine waposa wakunja
(Waposa wakunja) X2
Ndeno yahweh poti mukhala nane
Ine mantha ndilibe mantha ndilibe


VERSE 2

Kamba ka mantha
Uchimo nnaupasa mpata
Kusowa bata
Muntima mwanga

But when I read the verses that you wrote
Nnapeza mpumulo
Chondilimbitsa ntima
Nkudziwa kulikonse muli nane ine

Ndiopa ndani poti mwini wake wa moyo waine
Akonda ine!!!
Ndisowa chani poti mwini siliva ndi golide
Ali ndi ine!!!
So I just let him manifest
Through my words and my works
My talent was a blessing and a curse
Friday am in the club
Sunday kuyimba ku church

I had to change my ways
Cause I had numbers days
Nditatenga baibulo
Nawelenga salimo lidati


Ndingayende muchigwa cha nthuzi waimfa sindiopa
(Waimfa sindiopa)
Wankati ali mwaine waposa wakunja
(Waposa wakunja) X2
Ndeno yahweh poti mukhala nane
Ine mantha ndilibe mantha ndilibe