Song Page - Lyrify.me

Lyrify.me

Mpendadzuwa by Kay Sadik Lyrics

Genre: pop | Year: 2016

[VERSE 1]
Lija ndikale ndinkapanga zibwana
Ndichikondi
Poti tsuna yeni yeni yaine
Yimasowa
Eeya n'dakondapo ena wokongola
Koma chikondi chawo nakhala mbola
N'dakondanso wosandikonda
Wokonda chuma (wokonda chuma)
Koma iwe chibwelele
Moyo wanga unasinthaa
Ndati iwe chibwelele
Nzeru zanga zinakhwimaa

[ HOOK ]
Umandizula mtima
Ukamwetuliraaa Ukasekeleraaa
Iwe
Umafooketsa mphavu ya mdima
Ndiwe Chiphadzuwaaa
Ndiwe Mpendadzuwaa
Iwe Ndi Nyenyezi
[ VERSE 2 ]
Aliyense alinacho choyamikila inu
MULENGIyo
Ndiyamika pondipatsa iwe coz
Having you is not a joke
Ndiye ufusefuse ndi angati
Iwe ufufuze ndi angati
Wompeza wabwino wokhulupilika
Ndiwowelengekaa
N'chifukwa chake sindifuna
Kukutaya iwee
Ichi nchifukwa chake sindifuna
Kukunyoza iweeyoo

[ HOOK ]
Umandizula mtima
Ukamwetuliraaa Ukasekeleraaa
Iwe
Umafooketsa mphavu ya mdima
Ndiwe Chiphadzuwaaa
Ndiwe Mpendadzuwaa
Iwe Ndi Nyenyezi

[ BRIDGE ]
Iwe ukusiyana ndi enawaaa
Iwe ukusiyana ndi enawaaaa
You're so unique girl
Your lifestyle (is) real and simple
You're so unique girl
Your lifestyle (is) real and simple
[ HOOK ]
Umandizula mtima
Ukamwetuliraaa Ukasekeleraaa
Iwe
Umafooketsa mphavu ya mdima
Ndiwe Chiphadzuwaaa
Ndiwe Mpendadzuwaa
Iwe Ndi Nyenyezi