Iwe Ndi Ine by Kay Sadik Lyrics
(Intro)
Ooohwoouuoo woouuuwooo owoo
Ooohwoouuoo woouuuwooo owoo
Ohooo
[Verse 1]
Hunny.......
Ndili ndi nkhani yoti
Inu Ndi Ine…..Tingomvana.....
Ndine Munthu ndimalakwisa….sindukana......
Koma zomva imvazi ndima-dana nazo
Zokamba kambazi ndima-kwiya nazooo
Ngati pali vuto undidziwitse
Usawuze wanthu atiyaluse
Za ubale wathuwu sangathe (yeah)
Ndati sangathe iwoowa (coz)
Ndiwe wekha umandidziwa bho
Ndine ndekha nmakudziwanso
[Hook]
Mdziko lonseli ndimafuna
Iwe Ndi Ine, Eeeh, Iwe Ndi Iwe (mmmhu)
Pazokoma Zonsezi ndimakonda
Iwe Ndi Ine, mmmm, Iwe Ndi Ineyo (Ooohoo)
[Verse 2]
Am So Happy For us (for us)
Chiko-ndi umandipatsa nchapamwamba
Iwe ndi ine mpakampaka ukalamba uu
I love every moment that i spend with you
Ndiwe fupa lama fupa anga
I'll Die for you, am here for you baby
Zokhumba zanga ndiwe
Zokonda zanga ndiweyoo
[Hook]
Mdziko lonseli ndimafuna
Iwe Ndi Ine, Eeeh, Iwe Ndi Iwe (mmmhu)
Pazokoma Zonsezi ndimakonda
Iwe Ndi Ine, mmmm, Iwe Ndi Ineyo (Ooohoo)
[Verse 3]
Dziko lingawawe bwanji, ine ndili ndi iweyo
Tisalole wina apasule chikondi cha ifeyo
Kuwala ngati ngelo iwe (Nzakuveka velo inee)
Kuwala ngati ngelo iwe (Nzakuveka velo I Swear)
Uzipanga zisankho zakoo, Osati zanzakooo
Do what you feel is right (Yeah)
Kunama nama nama amanama
Koma timamvana afana timakhwana
Kunama nama nama amanama
Koma timamvana ifeyo timakwa-anaaa
Hook
Mdziko lonseli ndimafuna
Iwe Ndi Ine, Eeeh, Iwe Ndi Iwe (mmmhu)
Pazokoma Zonsezi ndimakonda
Iwe Ndi Ine, mmmm, Iwe Ndi Ineyo (Ooohoo) x2
[Outro]
Yeeeh iii yeeeeh